chat  learn 201 languages, create lessons

 SEARCH members    CREATE new lesson    READ lessons 

  Chewa - Nyanja lessons

	

color - la couleur

  kuda - black - noir   yera - white - blanc   chikasu - yellow - jaune   ndimwi - orange   wofiira - red - rouge   kamtambo - blue - bleu   abiriwiri - green - vert

numbers - les nombres

1 modzi 2 wiri 3 tatu 4 nayi 5 sanu 6 sanu n'chimodzi (5 and 1) 7 sanu n'ziwiri 8 sanu n'zitatu 9 sanu n'zinayi 10 khumi 11 khumi n'chimodzi (10 + 1) 12 khumi n'ziwiri (10 + 2) 20 makumi awiri (10 x 2) 30 makumi atatu (10 x 3) 100 chikwi chimodzi 1 000 zana limodzi half 1/2 theka less - kuchepera more + kuchulukira

days of the week - les jours de la semaine

Monday lolemba Tuesday lachiwiri Wednesday lachitatu Thursday lachinayi Friday lachisanu Saturday loweluka Sunday lamulungu, pasabata

time - le temps

What time is it? Nthawi ili bwanji ? midday, noon - twelufu koloko m'masana midnight - twelufu koloko m'usiku morning - m'mawa afternoon - masana evening - madzulo night - usiku day before yesterday - dzana yesterday - dzulo today lero tomorrow - mawa day(s) - tsiku (masiku) week(s) - mulungu (milungu) year(s) - chaka (zaka)

directions

right - kumanja left - kumanzere

food - la nourriture

(fresh) fruit - chipatso / zipatso (plur.) (fresh) vegetable - masamba salad - saladi beans - nyemba maize porridge - nsima rice - mpunga bread - buledi eggs - mazira fish - nsomba salt - mchere black pepper - tsabola water - madzi tea - tiyi coffee - khofi beer - mowa maize beer - masese maize drink - maheu cheap - kuchipa expensive - kudula

greetings - les salutations

hello - moni How are you? - Muli bwanji ? Fine, thank you - Ndili bwino And you? - Kaya inu/anzathu ? What is your name? - Dzina lanu ndani/ndi yani ? My name is ... Dzina langa ndi ... madam - amayi mister - abambo please - chonde thank you - zikomo yes - ee, eya, inde ("indeed") no - iyayi, ayi [respect] good morning - mwauka/mwadzuka bwanji? ... ndadzuka bwino (response) good afternoon - mwasewela bwanji? ... ndasewela bwino. (response) good evening - mwachoma bwanji ndachoma bwino (response) good night - usiku wabwino sleep well - gonani/mugone bwino goodbye, ("I'm going") - ndapita see you later - tionana I want - Ndikufuna I don't want - Sindikufuna I know - Ndimadziwa. I don't know - Sindidziwa. I don't understand - Sindimvetsa / Sindikumvetsa. I don't speak Nyanja - Sindimalankhula chinyanja Do you speak English? - Mumalankhula chizungu/chingelesi ? white person - mzungu / azungu (plur.) Indian - mmwenye / amwenye (plur.) I'm sorry - Pepani Help me! - Mundithandize ! Ndithadizeni ! Where is the toilet? - Chimbudzi chili kuti ? ladies (toilet) - chimbudzi cha akazi gents (toilet) - chimbudzi cha amuna